-
2 Samueli 3:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kodi Abineri mwana wa Nera simukumudziwa? Iye anabwera kuno kudzakupusitsani kuti adziwe zonse zokhudza inuyo ndiponso chilichonse chimene mukuchita.”
-