2 Samueli 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako anthu onse anabwera kwa Davide tsiku lomwelo masana kudzamʼpatsa chakudya kuti amutonthoze. Koma Davide analumbira kuti: “Mulungu andilange mowirikiza ngati ndingadye chakudya chilichonse dzuwa lisanalowe!”+
35 Kenako anthu onse anabwera kwa Davide tsiku lomwelo masana kudzamʼpatsa chakudya kuti amutonthoze. Koma Davide analumbira kuti: “Mulungu andilange mowirikiza ngati ndingadye chakudya chilichonse dzuwa lisanalowe!”+