2 Samueli 3:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anthu onse komanso Aisiraeli onse anadziwa tsiku limenelo kuti mfumu inalibe mlandu pa imfa ya Abineri mwana wa Nera.+
37 Anthu onse komanso Aisiraeli onse anadziwa tsiku limenelo kuti mfumu inalibe mlandu pa imfa ya Abineri mwana wa Nera.+