2 Samueli 3:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako mfumu inauza atumiki ake kuti: “Kodi simukudziwa kuti amene wafa leroyu ndi kalonga komanso munthu wamphamvu mu Isiraeli?+
38 Kenako mfumu inauza atumiki ake kuti: “Kodi simukudziwa kuti amene wafa leroyu ndi kalonga komanso munthu wamphamvu mu Isiraeli?+