2 Panali amuna awiri, omwe anali atsogoleri a magulu a achifwamba a mwana wa Sauli. Wina dzina lake anali Bana ndipo wina anali Rekabu. Onsewa anali ana a Rimoni wa ku Beeroti wa fuko la Benjamini. (Chifukwa dera la Beeroti+ linkaonedwanso kuti ndi gawo la fuko la Benjamini.