2 Samueli 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo analowa mʼnyumbamo ngati akufuna kukatenga tirigu, kenako anabaya Isi-boseti pamimba. Atatero, Rekabu ndi mchimwene wake Bana+ anathawa.
6 Iwo analowa mʼnyumbamo ngati akufuna kukatenga tirigu, kenako anabaya Isi-boseti pamimba. Atatero, Rekabu ndi mchimwene wake Bana+ anathawa.