-
2 Samueli 4:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iwo atalowa mʼnyumbamo, anapeza Isi-boseti atagona pabedi kuchipinda kwake ndipo anamubaya nʼkumupha. Kenako anamudula mutu nʼkuutenga ndipo anayenda usiku wonse mumsewu wopita ku Araba.
-