2 Samueli 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Davide ndi anthu onse amene anali naye ananyamuka nʼkupita ku Baale-yuda kuti akatenge Likasa la Mulungu woona.+ Pa likasa limeneli anthu amaitanirapo dzina la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+
2 Ndiyeno Davide ndi anthu onse amene anali naye ananyamuka nʼkupita ku Baale-yuda kuti akatenge Likasa la Mulungu woona.+ Pa likasa limeneli anthu amaitanirapo dzina la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+