2 Samueli 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi asilikali 20,000 oyenda pansi a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula* mahatchi onse a magaleta nʼkungosiya mahatchi 100.+
4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi asilikali 20,000 oyenda pansi a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula* mahatchi onse a magaleta nʼkungosiya mahatchi 100.+