-
2 Samueli 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho Toi anatumiza mwana wake Yoramu kwa Mfumu Davide kukamufunsa za moyo wake ndiponso kumuyamikira chifukwa chomenyana ndi Hadadezeri nʼkumugonjetsa. (Chifukwa Hadadezeri ankakonda kumenyana ndi Toi.) Popita kwa Davide, Yoramu anatenga zinthu zasiliva, zagolide ndi zakopa.
-