2 Samueli 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ziba anayankha mfumu kuti: “Zonse zimene mbuyanga mfumu mwandiuza, ine mtumiki wanu ndichita zomwezo.” Choncho Mefiboseti ankadya patebulo la Davide* ngati mmodzi wa ana a mfumu.
11 Ziba anayankha mfumu kuti: “Zonse zimene mbuyanga mfumu mwandiuza, ine mtumiki wanu ndichita zomwezo.” Choncho Mefiboseti ankadya patebulo la Davide* ngati mmodzi wa ana a mfumu.