2 Samueli 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Hanuni anatenga atumiki a Davide aja nʼkuwameta ndevu mbali imodzi,+ kenako anadula zovala zawo pakati moti zinalekeza mʼmatako nʼkuwauza kuti azipita.
4 Choncho Hanuni anatenga atumiki a Davide aja nʼkuwameta ndevu mbali imodzi,+ kenako anadula zovala zawo pakati moti zinalekeza mʼmatako nʼkuwauza kuti azipita.