2 Samueli 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Hadadezeri+ anatuma anthu kuti akatenge Asiriya amene anali mʼdera la ku Mtsinje.*+ Atatero anabwera ku Helamu ndipo Sobaki mkulu wa asilikali a Hadadezeri ndi amene ankawatsogolera.
16 Choncho Hadadezeri+ anatuma anthu kuti akatenge Asiriya amene anali mʼdera la ku Mtsinje.*+ Atatero anabwera ku Helamu ndipo Sobaki mkulu wa asilikali a Hadadezeri ndi amene ankawatsogolera.