2 Samueli 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkuwoloka Yorodano kupita ku Helamu. Ndiyeno Asiriya anayalana kuti akumane ndi Davide ndipo anayamba kumenyana naye.+
17 Davide atamva zimenezi, nthawi yomweyo anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkuwoloka Yorodano kupita ku Helamu. Ndiyeno Asiriya anayalana kuti akumane ndi Davide ndipo anayamba kumenyana naye.+