2 Samueli 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Asiriyawo anayamba kuthawa Isiraeli ndipo Davide anapha asilikali a Siriya 700 okwera magaleta komanso asilikali 40,000 okwera pamahatchi. Iye anaphanso Sobaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo la Siriya.+
18 Koma Asiriyawo anayamba kuthawa Isiraeli ndipo Davide anapha asilikali a Siriya 700 okwera magaleta komanso asilikali 40,000 okwera pamahatchi. Iye anaphanso Sobaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo la Siriya.+