-
2 Samueli 11:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zitatero, Davide anatumiza uthenga kwa Yowabu wakuti: “Umuuze Uriya Muhiti abwere.” Choncho Yowabu anauza Uriya kuti apite kwa Davide.
-