2 Samueli 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Davide anauza Uriya kuti: “Pita kunyumba kwako ukapume.”* Uriya atachoka mʼnyumba ya mfumu, mfumuyo inamutumizira mphatso.*
8 Kenako Davide anauza Uriya kuti: “Pita kunyumba kwako ukapume.”* Uriya atachoka mʼnyumba ya mfumu, mfumuyo inamutumizira mphatso.*