-
2 Samueli 11:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho anthu anauza Davide kuti: “Uriya sanapite kunyumba kwake.” Davide atamva zimenezi, anauza Uriya kuti: “Iweyo wayenda ulendo wautali, ndiye bwanji sunapite kunyumba kwako?”
-