-
2 Samueli 11:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Davide anauza Uriya kuti: “Leronso usanyamuke, upita mawa.” Choncho Uriya anakhalabe ku Yerusalemu tsiku limenelo ndiponso lotsatira.
-