-
2 Samueli 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Davide anamuitana kuti adzadye ndi kumwa naye limodzi ndipo anamuledzeretsa. Koma madzulo Uriya anapita kukagona pabedi limodzi ndi atumiki a mbuye wake, ndipo sanapite kunyumba kwake.
-