-
2 Samueli 11:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 mwina mfumu ikakwiya ndipo ikakufunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani mumamenya nkhondo moyandikira mzindawo kwambiri choncho? Simumadziwa kuti akuponyerani mivi kuchokera pamwamba pa mpanda?
-