-
2 Samueli 11:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno munthuyo anauza Davide kuti: “Asilikali awo anali amphamvu kuposa ife, ndipo anabwera kudzamenyana nafe kutchire, koma tinayesetsa kulimbana nawo mpaka anabwerera kugeti la mzinda.
-