2 Samueli 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma asilikali ena amaponya mivi kuchokera pamwamba pa mpanda nʼkumabaya atumiki anu, moti atumiki anu ena a mfumu, afa. Nayenso mtumiki wanu Uriya Muhiti, wafa.”+
24 Koma asilikali ena amaponya mivi kuchokera pamwamba pa mpanda nʼkumabaya atumiki anu, moti atumiki anu ena a mfumu, afa. Nayenso mtumiki wanu Uriya Muhiti, wafa.”+