-
2 Samueli 12:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma munthu wosauka uja anali ndi kamwana ka nkhosa kamodzi kokha kakakazi kamene anagula.+ Iye ankasamalira kamwana ka nkhosako ndipo kankakulira limodzi ndi ana ake. Kankhosako kankadya limodzi ndi munthuyo chakudya chochepa chomwe anali nacho komanso kankamwa naye limodzi. Kankagonanso mʼmanja mwake ndipo kankangokhala ngati mwana wake wamkazi.
-