2 Samueli 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno kwa munthu wolemera uja kunabwera mlendo. Koma munthu wolemerayo sanatenge nkhosa kapena ngʼombe yake kuti akonzere chakudya mlendoyo. Mʼmalomwake, anatenga kamwana ka nkhosa ka munthu wosauka uja nʼkuphera mlendoyo.”+
4 Ndiyeno kwa munthu wolemera uja kunabwera mlendo. Koma munthu wolemerayo sanatenge nkhosa kapena ngʼombe yake kuti akonzere chakudya mlendoyo. Mʼmalomwake, anatenga kamwana ka nkhosa ka munthu wosauka uja nʼkuphera mlendoyo.”+