2 Samueli 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Davide atamva zimenezi anamukwiyira kwambiri munthuyo ndipo anauza Natani kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo,+ munthu amene anachita zimenezi ayenera kufa! 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Nsanja ya Olonda,5/1/2010, tsa. 30
5 Davide atamva zimenezi anamukwiyira kwambiri munthuyo ndipo anauza Natani kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo,+ munthu amene anachita zimenezi ayenera kufa!