2 Samueli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iweyo unachita zimenezi mobisa,+ koma ine ndidzazichita masana Aisiraeli onse akuona.’”