-
2 Samueli 12:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako Natani anapita kunyumba kwake.
Ndiyeno Yehova anachititsa kuti mwana amene mkazi wa Uriya anaberekera Davide ayambe kudwala.
-