-
2 Samueli 12:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Pa tsiku la 7, mwanayo anamwalira. Koma atumiki a Davide ankaopa kumuuza kuti mwanayo wamwalira. Iwo ankanena kuti: “Mwanayu ali moyo, tinalankhula naye Davide koma sanatimvere. Ndiye timuuza bwanji kuti mwana uja wamwalira? Tikamuuza akhoza kuchita chinachake choipa.”
-