-
2 Samueli 12:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Davide ataona kuti atumiki ake akunongʼonezana, anazindikira kuti mwana uja wamwalira. Choncho anafunsa atumiki akewo kuti: “Kodi mwana uja wamwalira?” Iwo anamuyankha kuti: “Inde wamwalira.”
-