-
2 Samueli 12:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atumiki ake anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwachita zimenezi? Mwanayu ali moyo, mumakana chakudya ndiponso mumalira. Koma atangomwalira, mwadzuka nʼkuyamba kudya.”
-