2 Samueli 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Yowabu anatumiza anthu kuti akauze Davide kuti: “Ndamenyana ndi mzinda wa Raba+ ndipo ndalanda mzinda wa madzi.*
27 Choncho Yowabu anatumiza anthu kuti akauze Davide kuti: “Ndamenyana ndi mzinda wa Raba+ ndipo ndalanda mzinda wa madzi.*