30 Kenako anatenga chipewa chachifumu chimene chinali kumutu kwa Malikamu ndipo anthu anaveka Davide chipewacho. Kulemera kwake kunali kofanana ndi talente imodzi ya golide, ndi miyala yamtengo wapatali. Iye anatenganso zinthu zambirimbiri+ mumzindawo.+