-
2 Samueli 14:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mayi wa ku Tekowayo anapita kukaonana ndi mfumu, ndipo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi, kenako anadzigwetsa, nʼkunena kuti: “Chonde mfumu ndithandizeni!”
-