-
2 Samueli 14:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ine mtumiki wanu ndinali ndi ana awiri aamuna. Tsiku lina anawo ali kutchire anayamba kumenyana ndipo panalibe wowaleretsa. Ndiyeno wina anapha mnzake.
-