-
2 Samueli 14:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Panopa banja lonse landiukira ine mtumiki wanu ndipo aliyense akunena kuti, ‘Bweretsa wopha mchimwene wakeyo kuti timuphe chifukwa cha mchimwene wake amene anamupha.+ Kaya zimenezi zipangitsa kuti pasakhale wolandira cholowa, palibe vuto.’ Anthuwa adzazimitsa khala limene latsala ndipo adzasiya mwamuna wanga wopanda dzina komanso mbewu yotsala padziko lapansi.”
-