-
2 Samueli 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mayi wa ku Tekowayo anauza mfumu kuti: “Mbuyanga mfumu, wolakwa ndikhale ine ndi anthu amʼnyumba ya bambo anga, koma inu mfumu, ndi mpando wanu wachifumu, ndinu osalakwa.”
-