-
2 Samueli 14:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako mfumu inanena kuti: “Ngati aliyense angalankhule nawenso za nkhani imeneyi, ubwere naye kwa ine ndipo sadzakuvutitsanso.”
-