-
2 Samueli 14:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno mkaziyo anati: “Mbuyanga mfumu, chonde ndiloleni ine mtumiki wanu kuti ndikuuzeni mawu amodzi.” Mfumu inamuuza kuti: “Lankhula!”
-