2 Samueli 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mayiyo ananena kuti: “Nʼchifukwa chiyani inu mfumu mwachitira anthu a Mulungu zinthu ngati zimenezi?+ Zimene inu mfumu mwalankhulazi, zikusonyeza kuti ndinu wolakwa chifukwa munathamangitsa mwana wanu ndipo simunamuitanitse kuti abwerenso.+
13 Mayiyo ananena kuti: “Nʼchifukwa chiyani inu mfumu mwachitira anthu a Mulungu zinthu ngati zimenezi?+ Zimene inu mfumu mwalankhulazi, zikusonyeza kuti ndinu wolakwa chifukwa munathamangitsa mwana wanu ndipo simunamuitanitse kuti abwerenso.+