-
2 Samueli 14:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndabwera kudzakuuzani zimenezi mbuyanga mfumu chifukwa anthu andichititsa mantha. Moti ine mtumiki wanu ndinati, ‘Bwanji ndikalankhule ndi mfumu. Mwina mfumu idzamvera zimene kapolo wake wapempha.
-