2 Samueli 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu ikhoza kundimvera nʼkundipulumutsa kwa munthu amene akufuna kupha ineyo komanso mwana wanga mmodzi yekhayo kuti tisalandire cholowa chomwe Mulungu anatipatsa.’+
16 Mfumu ikhoza kundimvera nʼkundipulumutsa kwa munthu amene akufuna kupha ineyo komanso mwana wanga mmodzi yekhayo kuti tisalandire cholowa chomwe Mulungu anatipatsa.’+