-
2 Samueli 14:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiye ine mtumiki wanu ndinati, ‘Mawu a mbuyanga mfumu anditonthoze,’ popeza inu mbuyanga muli ngati mngelo wa Mulungu woona, posiyanitsa chabwino ndi choipa. Yehova Mulungu wanu akhale nanu.”
-