-
2 Samueli 14:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno mfumu inauza mayiyo kuti: “Usandibisire chilichonse pa zimene ndikufuna kukufunsa.” Mayiyo ananena kuti: “Lankhulani mbuyanga mfumu.”
-