2 Samueli 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Abisalomu ankameta tsitsi lake kumapeto kwa chaka chilichonse chifukwa linkamulemera kwambiri. Ndipo akameta tsitsi lakelo, linkalemera masekeli 200* akaliyeza ndi mwala wachifumu woyezera kulemera kwa zinthu.*
26 Abisalomu ankameta tsitsi lake kumapeto kwa chaka chilichonse chifukwa linkamulemera kwambiri. Ndipo akameta tsitsi lakelo, linkalemera masekeli 200* akaliyeza ndi mwala wachifumu woyezera kulemera kwa zinthu.*