2 Samueli 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Abisalomu anakhala ku Yerusalemu zaka ziwiri zathunthu koma sanaonane ndi mfumu.+