-
2 Samueli 14:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Kenako, Abisalomu anaitanitsa Yowabu kuti amutume kwa mfumu, koma Yowabu sanapite kwa Abisalomu. Iye anamuitanitsanso kachiwiri, koma anakana.
-