2 Samueli 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Davide anauza Abisai ndi atumiki ake onse kuti: “Ngati mwana wanga weniweni, wobereka ndekha akufunafuna moyo wanga,+ kuli bwanji munthu wa fuko la Benjaminiyu?+ Musiyeni anyoze, chifukwa Yehova ndi amene wamuuza. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:11 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, tsa. 32
11 Kenako Davide anauza Abisai ndi atumiki ake onse kuti: “Ngati mwana wanga weniweni, wobereka ndekha akufunafuna moyo wanga,+ kuli bwanji munthu wa fuko la Benjaminiyu?+ Musiyeni anyoze, chifukwa Yehova ndi amene wamuuza.