2 Samueli 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abisalomu ndi amuna onse a Isiraeli, anafika ku Yerusalemu ndipo Ahitofeli+ anali naye limodzi.