-
2 Samueli 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Husai anayankha Abisalomu kuti: “Ayi, ine ndili kumbali ya munthu amene wasankhidwa ndi Yehova komanso amene wasankhidwa ndi anthu awa ndiponso amuna onse a mu Isiraeli. Ine ndidzakhala ndi ameneyo.
-